1 Samueli 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo malipiro onoletsera mapulawo, makasu, mafoloko a mano atatu ndi nkhwangwa, ndiponso kukonza chisonga chotosera ngʼombe anali pimu* imodzi. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2154 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 29
21 Ndipo malipiro onoletsera mapulawo, makasu, mafoloko a mano atatu ndi nkhwangwa, ndiponso kukonza chisonga chotosera ngʼombe anali pimu* imodzi.