1 Samueli 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Alonda a Sauli ku Gibeya+ wa ku Benjamini anaona kuti paliponse mumsasamo pali chipwirikiti.+