-
1 Samueli 14:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pa nthawi imene Sauli ankalankhula ndi wansembe, chipwirikiti chinkawonjezeka kwambiri mumsasa wa Afilisiti. Kenako Sauli anauza wansembeyo kuti: “Basi, siya zimene ukuchitazo.”
-