-
1 Samueli 14:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Sauli ndi anthu onse amene anali naye anasonkhana nʼkupita kukamenyana ndi Afilisiti. Atafika kumeneko anapeza kuti Afilisiti akumenyana okhaokha ndi malupanga, moti kunali chisokonezo chosaneneka.
-