1 Samueli 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake ankalumbirira anthu,+ moti anagwiritsa ntchito ndodo yake kutenga uchi pangʼono pachisa. Kenako anadya uchiwo ndipo atatero, anayera mʼmaso. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:27 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 22
27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake ankalumbirira anthu,+ moti anagwiritsa ntchito ndodo yake kutenga uchi pangʼono pachisa. Kenako anadya uchiwo ndipo atatero, anayera mʼmaso.