1 Samueli 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno munthu wina anamuuza kuti: “Bambo ako alumbirira anthu mwamphamvu kuti, ‘Munthu aliyense amene adye chakudya lero ndi wotembereredwa.’+ Nʼchifukwa chake anthuwa atopa kwambiri.”
28 Ndiyeno munthu wina anamuuza kuti: “Bambo ako alumbirira anthu mwamphamvu kuti, ‘Munthu aliyense amene adye chakudya lero ndi wotembereredwa.’+ Nʼchifukwa chake anthuwa atopa kwambiri.”