-
1 Samueli 14:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Yonatani anayankha kuti: “Bambo anga achititsa kuti anthu avutike kwambiri. Taonani mmene maso anga ayerera nditangolawa uchi pangʼono.
-