1 Samueli 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno anthu ena anauza Sauli kuti: “Anthutu akuchimwira Yehova. Akudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Iye anati: “Mwachita zinthu mopanda chikhulupiriro. Gubuduzani chimwala mubwere nacho kuno mwamsanga.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:33 Nsanja ya Olonda,4/15/1994, tsa. 31
33 Ndiyeno anthu ena anauza Sauli kuti: “Anthutu akuchimwira Yehova. Akudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Iye anati: “Mwachita zinthu mopanda chikhulupiriro. Gubuduzani chimwala mubwere nacho kuno mwamsanga.”