-
1 Samueli 14:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako Sauli anati: “Tiyeni tipite kwa Afilisiti usiku kukamenyana nawo ndipo tikalande zinthu zawo mpaka mʼmawa. Tisakasiye munthu aliyense wamoyo.” Anthuwo anayankha kuti: “Chitani chilichonse chimene mukuona kuti nʼchabwino.” Ndiyeno wansembe anati: “Tiyeni tifunse Mulungu woona pamalo omwe ano.”+
-