1 Samueli 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Sauli anafunsa Mulungu kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka mʼmanja mwa Aisiraeli?” Koma pa tsikuli Mulungu sanamuyankhe.
37 Kenako Sauli anafunsa Mulungu kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka mʼmanja mwa Aisiraeli?” Koma pa tsikuli Mulungu sanamuyankhe.