-
1 Samueli 14:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Ndiyeno Sauli anauza Aisiraeli onse kuti: “Inuyo mukhale kumbali ina, ndipo ine ndi mwana wanga Yonatani tikhalanso ku mbali ina.” Anthuwo anauza Sauli kuti: “Chitani zimene mukuona kuti nʼzabwino.”
-