1 Samueli 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno Sauli anauza Yehova kuti: “Inu Mulungu wa Isiraeli, tiyankheni kudzera mwa Tumimu!”+ Atatero, Yonatani ndi Sauli anasankhidwa ndipo anthuwo anaoneka kuti alibe mlandu.
41 Ndiyeno Sauli anauza Yehova kuti: “Inu Mulungu wa Isiraeli, tiyankheni kudzera mwa Tumimu!”+ Atatero, Yonatani ndi Sauli anasankhidwa ndipo anthuwo anaoneka kuti alibe mlandu.