1 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anandituma kudzakudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu ake Aisiraeli.+ Ndiye tamvera zimene Yehova wanena.+
15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anandituma kudzakudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu ake Aisiraeli.+ Ndiye tamvera zimene Yehova wanena.+