1 Samueli 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ndibwezera Aamaleki chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli polimbana nawo pamene Aisiraeliwo ankachokera ku Iguputo.+
2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ndibwezera Aamaleki chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli polimbana nawo pamene Aisiraeliwo ankachokera ku Iguputo.+