1 Samueli 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Samueli atadzuka mʼmamawa kuti akaonane ndi Sauli, anamva kuti: “Sauli anapita ku Karimeli+ ndipo wamangako chipilala kuti anthu azimukumbukira,+ kenako wapita ku Giligala.”
12 Samueli atadzuka mʼmamawa kuti akaonane ndi Sauli, anamva kuti: “Sauli anapita ku Karimeli+ ndipo wamangako chipilala kuti anthu azimukumbukira,+ kenako wapita ku Giligala.”