1 Samueli 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samueli anauza Sauli kuti: “Khala chete! Dikira ndikuuze zimene Yehova wandiuza usiku wapitawu.”+ Sauli anayankha kuti: “Lankhulani!”
16 Samueli anauza Sauli kuti: “Khala chete! Dikira ndikuuze zimene Yehova wandiuza usiku wapitawu.”+ Sauli anayankha kuti: “Lankhulani!”