1 Samueli 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunkadziona ngati wachabechabe+ utasankhidwa kukhala mtsogoleri wa mafuko a Isiraeli komanso pamene Yehova anakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?+
17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunkadziona ngati wachabechabe+ utasankhidwa kukhala mtsogoleri wa mafuko a Isiraeli komanso pamene Yehova anakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?+