1 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye nʼchifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira kutenga zinthu zawo mwadyera+ nʼkuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”
19 Ndiye nʼchifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira kutenga zinthu zawo mwadyera+ nʼkuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”