1 Samueli 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera mawu a Yehova. Ndagwira ntchito imene Yehova anandituma ndipo ndabweretsa Agagi mfumu ya Amaleki, koma Aamalekiwo ndawapha.+
20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera mawu a Yehova. Ndagwira ntchito imene Yehova anandituma ndipo ndabweretsa Agagi mfumu ya Amaleki, koma Aamalekiwo ndawapha.+