-
1 Samueli 15:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Pamene Samueli ankatembenuka kuti azipita, Sauli anagwira mʼmunsi mwa mkanjo wodula manja wa Samueli ndipo mkanjowo unangʼambika.
-