1 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Samueli anati: “Mʼbweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mokayikira.* Mumtima mwake ankaganiza kuti: ‘Panopa pondipha ndiye padutsa.’
32 Kenako Samueli anati: “Mʼbweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mokayikira.* Mumtima mwake ankaganiza kuti: ‘Panopa pondipha ndiye padutsa.’