1 Samueli 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo* kuti akamenye nkhondo. Anasonkhana ku Soko+ mʼdera la Yuda ndipo anamanga msasa wawo pakati pa Soko ndi Azeka+ ku Efesi-damimu.+
17 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo* kuti akamenye nkhondo. Anasonkhana ku Soko+ mʼdera la Yuda ndipo anamanga msasa wawo pakati pa Soko ndi Azeka+ ku Efesi-damimu.+