1 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfilisitiyo anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikunyoza asilikali a Isiraeli+ lero. Ndipatseni munthu woti ndimenyane naye!”
10 Mfilisitiyo anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikunyoza asilikali a Isiraeli+ lero. Ndipatseni munthu woti ndimenyane naye!”