1 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Jese anauza mwana wake Davide kuti: “Tenga tirigu wokazinga uyu wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mikate 10, ndipo upite nazo mofulumira kwa azichimwene ako kumsasa.
17 Kenako Jese anauza mwana wake Davide kuti: “Tenga tirigu wokazinga uyu wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mikate 10, ndipo upite nazo mofulumira kwa azichimwene ako kumsasa.