1 Samueli 17:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Choncho Davide atangofika kuchokera komwe anapha Mfilisiti, Abineri anamutenga nʼkupita naye kwa Sauli, mutu wa Mfilisiti+ uja uli mʼmanja.
57 Choncho Davide atangofika kuchokera komwe anapha Mfilisiti, Abineri anamutenga nʼkupita naye kwa Sauli, mutu wa Mfilisiti+ uja uli mʼmanja.