1 Samueli 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Davide anayankha Sauli kuti: “Ndine ndani ine ndipo abale anga ndi anthu a mʼbanja la bambo anga ndi ndani mu Isiraeli, kuti ndikhale mkamwini wa mfumu?”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:18 Nsanja ya Olonda,4/1/2004, tsa. 15
18 Koma Davide anayankha Sauli kuti: “Ndine ndani ine ndipo abale anga ndi anthu a mʼbanja la bambo anga ndi ndani mu Isiraeli, kuti ndikhale mkamwini wa mfumu?”+