-
1 Samueli 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kuwonjezera pamenepo, Sauli analamula atumiki ake kuti: “Mukalankhule ndi Davide mwachinsinsi ndipo mukamuuze kuti, ‘Mfumutu ikusangalala nawe, ndipo atumiki ake onse akukukonda kwambiri. Ndiye chita mgwirizano wa ukwati ndi mfumu.’”
-