1 Samueli 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atumiki a Sauli atauza Davide mawu amenewa, Davide anawayankha kuti: “Kodi mukuona ngati ndi nkhani yaingʼono kuti munthu wosauka ndi wonyozeka ngati ine ndichite mgwirizano wa ukwati ndi mfumu?”+
23 Atumiki a Sauli atauza Davide mawu amenewa, Davide anawayankha kuti: “Kodi mukuona ngati ndi nkhani yaingʼono kuti munthu wosauka ndi wonyozeka ngati ine ndichite mgwirizano wa ukwati ndi mfumu?”+