1 Samueli 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho atumiki a Sauli anauza Davide uthengawu. Davide anasangalala nazo ndipo anavomera kuti achite mgwirizano wa ukwati ndi mfumu.+ Nthawi imene anagwirizana isanakwane,
26 Choncho atumiki a Sauli anauza Davide uthengawu. Davide anasangalala nazo ndipo anavomera kuti achite mgwirizano wa ukwati ndi mfumu.+ Nthawi imene anagwirizana isanakwane,