1 Samueli 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, Yonatani anaitana Davide nʼkumufotokozera zonse. Kenako, Yonatani anatenga Davide nʼkupita naye kwa Sauli ndipo Davide anapitiriza kukhala ndi Sauli ngati poyamba.+
7 Zitatero, Yonatani anaitana Davide nʼkumufotokozera zonse. Kenako, Yonatani anatenga Davide nʼkupita naye kwa Sauli ndipo Davide anapitiriza kukhala ndi Sauli ngati poyamba.+