1 Samueli 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Mikala anatenga fano la terafi* nʼkuliika pabedi. Iye anaika neti yaubweya wa mbuzi pamene Davide ankatsamiritsa mutu wake ndipo anafunditsa fanolo chovala. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:13 Nsanja ya Olonda,6/1/2004, tsa. 29
13 Ndiyeno Mikala anatenga fano la terafi* nʼkuliika pabedi. Iye anaika neti yaubweya wa mbuzi pamene Davide ankatsamiritsa mutu wake ndipo anafunditsa fanolo chovala.