1 Samueli 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthuwo atalowa, anapeza fano la terafi* lili pabedi, neti yaubweya wa mbuzi ili pamene pakanakhala mutu wa Davide.
16 Anthuwo atalowa, anapeza fano la terafi* lili pabedi, neti yaubweya wa mbuzi ili pamene pakanakhala mutu wa Davide.