1 Samueli 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yonatani anamuyankha kuti: “Nʼzosatheka zimenezo,+ suufa. Bambo anga sangachite chilichonse, kaya chachikulu kapena chachingʼono, osandiuza. Ndiye bambo anga angandibisire nkhani imeneyi chifukwa chiyani? Sizingachitike zimenezo.”
2 Yonatani anamuyankha kuti: “Nʼzosatheka zimenezo,+ suufa. Bambo anga sangachite chilichonse, kaya chachikulu kapena chachingʼono, osandiuza. Ndiye bambo anga angandibisire nkhani imeneyi chifukwa chiyani? Sizingachitike zimenezo.”