-
1 Samueli 20:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yonatani anauza Davide kuti: “Ndidzalankhula ndi bambo anga mawa kapena mkuja ndipo Yehova Mulungu wa Isiraeli akhale mboni. Ngati alibe nawe chifukwa, ndikutumizira uthenga wokudziwitsa.
-