1 Samueli 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo mkuja ayenera kuti adzafunsa za iweyo. Udzapite kukabisala pamalo amene unabisala tsiku lijali* ndipo udzakhale pafupi ndi mwala uwu.
19 Ndipo mkuja ayenera kuti adzafunsa za iweyo. Udzapite kukabisala pamalo amene unabisala tsiku lijali* ndipo udzakhale pafupi ndi mwala uwu.