-
1 Samueli 20:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma ndikadzauza mnyamatayo kuti, ‘Mivi ili kutali kwambiri ndi iwe,’ ndiye kuti uyenera kuchoka, chifukwa Yehova wakulola kupita.
-