1 Samueli 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inakhala pamalo ake a nthawi zonse, pafupi ndi khoma. Yonatani anakhala moyangʼanizana ndi mfumuyo, pamene Abineri+ anakhala pambali pa mfumu. Koma mpando wa Davide unali wopanda munthu.
25 Inakhala pamalo ake a nthawi zonse, pafupi ndi khoma. Yonatani anakhala moyangʼanizana ndi mfumuyo, pamene Abineri+ anakhala pambali pa mfumu. Koma mpando wa Davide unali wopanda munthu.