1 Samueli 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku limeneli Sauli sananene chilichonse, chifukwa ankaganiza kuti: ‘Chinachake chachitika ndipo wadetsedwa.+ Ayenera kuti wadetsedwa ndithu.’
26 Pa tsiku limeneli Sauli sananene chilichonse, chifukwa ankaganiza kuti: ‘Chinachake chachitika ndipo wadetsedwa.+ Ayenera kuti wadetsedwa ndithu.’