-
1 Samueli 20:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Koma Sauli anamukwiyira kwambiri Yonatani, ndipo anamuuza kuti: “Chimwana cha mkazi wopanduka iwe! Ukuganiza sindikudziwa kuti wasankha kugwirizana ndi mwana wa Jese, nʼkudzichititsa manyazi wekha ndiponso kuvula mayi ako?
-