1 Samueli 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi yomweyo, Yonatani ananyamuka patebulopo atakwiya kwambiri, ndipo tsiku limeneli* sanadye. Iye anachita zimenezi chifukwa chopsa mtima ndi nkhani ya Davide+ komanso chifukwa bambo ake anamʼchititsa manyazi.
34 Nthawi yomweyo, Yonatani ananyamuka patebulopo atakwiya kwambiri, ndipo tsiku limeneli* sanadye. Iye anachita zimenezi chifukwa chopsa mtima ndi nkhani ya Davide+ komanso chifukwa bambo ake anamʼchititsa manyazi.