-
1 Samueli 20:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno anauza mnyamata wakeyo kuti: “Thamanga ukatole mivi imene ndikuponya.” Mnyamatayo anathamanga, ndipo Yonatani anaponya muvi moti unamupitirira.
-