-
1 Samueli 20:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Mnyamata uja atafika pamalo amene muvi wa Yonatani unagwera, Yonatani anafuula kuti: “Muvi wagwera patali kutsogolo kwako!”
-