-
1 Samueli 20:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Yonatani anapitiriza kuti: “Fulumira! Thamanga, usachedwe!” Ndiyeno mnyamatayo anatola miviyo nʼkupita nayo kwa mbuye wakeyo.
-