-
1 Samueli 21:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kodi ine ndikusowa anthu amisala kuti mundibweretsere munthu ameneyu kudzachita zamisala kunoko? Kodi ameneyu ndi woyenera kulowa mʼnyumba mwanga?”
-