-
1 Samueli 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Nthawi yomweyo mfumu inatumiza anthu kuti akaitane Ahimeleki wansembe, mwana wa Ahitubu komanso ansembe onse amʼnyumba ya bambo ake omwe anali ku Nobu. Choncho onse anabwera kwa mfumu.
-