-
1 Samueli 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Sauli anapitiriza kumuuza kuti: “Nʼchifukwa chiyani iweyo ndi mwana wa Jese mwandikonzera chiwembu? Iweyo unamʼpatsa mkate ndi lupanga komanso unamufunsira kwa Mulungu. Iye wandiukira ndipo panopa wandibisalira.”
-