1 Samueli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi ndayamba lero kumufunsira kwa Mulungu?+ Sindingachite zimene mukunenazo! Chonde mfumu musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu ndiponso anthu onse amʼnyumba ya bambo anga, chifukwa ine mtumiki wanu sindinadziwe chilichonse pa nkhaniyi.”+
15 Kodi ndayamba lero kumufunsira kwa Mulungu?+ Sindingachite zimene mukunenazo! Chonde mfumu musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu ndiponso anthu onse amʼnyumba ya bambo anga, chifukwa ine mtumiki wanu sindinadziwe chilichonse pa nkhaniyi.”+