1 Samueli 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mfumu inati: “Ufa ndithu+ Ahimeleki, iweyo ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ako.”+