1 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi, anthu anauza Davide kuti: “Afilisiti akumenyana ndi mzinda wa Keila,+ ndipo akulanda zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”
23 Patapita nthawi, anthu anauza Davide kuti: “Afilisiti akumenyana ndi mzinda wa Keila,+ ndipo akulanda zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”