1 Samueli 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma amuna amene anali ndi Davide ananena kuti: “Ngati tikuchita mantha tili ku Yuda kuno,+ ndiye kuli bwanji tikapita ku Keila kukamenyana ndi asilikali a Afilisiti!”+
3 Koma amuna amene anali ndi Davide ananena kuti: “Ngati tikuchita mantha tili ku Yuda kuno,+ ndiye kuli bwanji tikapita ku Keila kukamenyana ndi asilikali a Afilisiti!”+